Ochita chisudzo Bonzo ndi Jubeki
∙ Khoswe: woyang’anira akaidi ku ndende
10
∙ Goli: Wamkulu wapolisi
∙ Anne: Mkazi wa Gole
∙ Mayi khoswe: Mkazi wa Khoswe
∙ Mlonda
∙ Apolisi asanu
∙ Woweruza milandu
∙ Anthu omvera milandu
Malo mwachidule
∙ Kunyumba kwa Goli
∙ Kundende
∙ Kunyumba kwa mzimayi wogulitsa mowa
∙ Kumanda komwe kudabisidwa ndalama
∙ Panjira (pamene Bonzo ndi Jubeki adasinthira zovala) Kubwalo lamilandu Kunyumba kwa Khoswe
∙ Kuncthito kwa Goli