Gwero lachisudzo
∙ Mchira wabuluzi womwe udapezeka m’chipanda chamowa womwe Nadzonzi adatenga kwa Nasiwelo ndipo adampatsa mamuna wake Ndileya
Ochita chisudzo
- Ndileya: Mwamuna wa Nadzonzi
- Nadzonzi : Mkazi wa Ndileya
- Chidazi: Malume a Nadzonzi
- Nachuma: Mchemwali wamkulu wa Nadzonzi
- Amfumu
- Anthu
Malo mwachidule
▪ Kunyumba kwa Ndileya ndi Nadzonzi
▪ Kuchitsime
▪ Kunyumba kwa Nasiwelo
▪ Ku Zomba (kuchipatala cha anthu amisala)
▪ Kunyumba kwa a Chidazi
▪ Ku bwalo lamilandu (kwa amfumu)