Ochita chisudzo
∙ Mgezenge: Munthu wolemera wa zaka makumi asani ndi limodzi
∙ Nagama: Mkazi wa Mgezenge wa zaka 45
∙ Gama ndi Abiti: Bambo wa Nagama
∙ Abiti: Mkazi wa Gama
∙ Zikani: Mwana wa Gama
∙ Chisomo: Mnzake wa Zikani
∙ Funsani : Mnyamata wogulitsa mu golosale ya Mgezenge
∙ Mayamiko: Mnyamata wamng’ono
∙ Mfumu ya m’mudzi
∙ Kamwendo: Tenanti wa pa esiteti
Malo mwachidule
▪ Kunyumba kwa Mgezenge ndi Nagama
▪ Kunyumba kwa makolo a Zikani
▪ Kunkhalango komwe ankakhala Zikani ndi Chisomo
▪ Kusukulu
▪ Ku esiteti
▪ Kunyumba kwa Zikani ndi Funsani
▪ Kugolosale ya Mgezenge
▪ Kunyumba kwa a Kamwendo
▪ Mudzi woyandikana ndi nkhalango