Ochita chisudzo
∙ Mfumu Tandwe: Mfumu ya m’mudzi
∙ Bambo Tikita: Nduna yayikulu ya mfumu
∙ Bambo Sefani: Nduna ya mfumu
∙ Mayi Amuli: Nduna ya mfumu omwe inkayang’anira za achinyamata komanso kuonetsetsa kuti pasamakhale kusalana
∙ Bambo Lungu: Nduna ya mfumu yomwe inkayang’anira za nkhanza zochitika kwa amayi ndi ana aakazi
∙ Mayi Chibwe: Nduna ya mfumu yomwe inkayang’anira zachilengedwe ∙ Mayi Mwenda: Nduna ya mfumu
∙ Gogo Tsinde: Mlangizi wamkulu wa mfumu
∙ Chiphaliwali: Mtumiki wa mfumu yemwe amakhazikitsa bata panthawi ya mkumano/msonkhano pabwalo la mfumu
∙ Oyimira magulu osiyanasiyana m’mudzi
∙ Anthu am’mudzi
Malo mwachidule
∙ Kubwalo lamfumu
∙ Kupolisi