Course Content
Kufunika kwa Zisudzo
Chisudzo ndi nkhani yochitika kapena yopeka yomwe imafotokoza zinthu mokhala ngati zikuchitika kumene.
0/2
MITU YONSE MNKHANIYI
0/1
Khoswe Wa Padenga
Kukamba za Bonzo, Goli, Khoswe, Anne ndi Jubeki
0/2
Mudzi Wa Mfumu Tandwe
Kuonongeka kwa zachilengedwe ndi mavuto ena
0/3
CHAMDOTHE NDI ZISUDZO ZINA

Kufunika kwa zisudzo  

  1. Kudziwitsa 
  2. Kuphunzitsa 
  3. Kudzudzula 
  4. Kuchenjeza 
  5. Kusangalatsa 
  6. Kuyamikira 

Magwero  

  1. Mbiri yakale 
  2. Ndale  
  3. Ulamuliro wosiyanasiyana  
  4. Miyambo ndi chikhalidwe  
  5. Udindo  

Kayankhulidwe  

Kachibadwidwe (kukweza/kutsitsa mawu)  

Kudziyankhulira  

Kukambirana ndi ena  

Kuyankhula m’zining’a, mikuluwiko ndi mizimbayitso  

Kuzukuta chisudzo  

Mtengambali  

Malo ndi nthawi  

Mfundo yayikulu  

Tsatanetsatane wa nkhani (plot)  

Chiyambi (introduction/exposition)  

Chikweza (rising action)  

Pampondachimera (climax)  

Mtsetse (falling action)  

Mathero a nkhani (resolution)  

Chiyankhulo ndi nsetso (style)  

Zina zoyenera kudziwa m’chisudzo  

Gawo la chisudzo (act)  

Mtengambali (actor)  

Mpangankhani wotsutsa (antagonist) 

Mpangankhani wamkulu (protagonist)  

Zochitika (action)  

Gwero ndi zotsatira (cause and effect)  

Maonetsedwe a mpangankhani (characterisation)  

Chisokonezo(conflict)  

Kulimbana (Complication)  

Ochita chisudzo (dramatis personae)  

Mkwanguliro (epilogue)  

Mpanduki (foil)  

Msemphano (irony)  

Nunsu ya chisudzo (scene)  

Kudziyankhulitsa (soliloque)  

Kuchita chisudzo mwachinunu (miming)  

error: Content is protected !!
Scroll to Top