Wolemba: (Mufunanji Magalasi) Womasulira: (Wisdom Nkhoma)
Ochita chisudzo
1. Chamdothe: Mwana wa dongo wa Ndatopa
2. Ndatopa: Amake Chamdothe
3. Angozo : Mwamuna wa Ndatopa
4. Mayi Lunda: Mnzawo wa Ndatopa
5. Zione: Mtsikana wokondana kwambiri ndi Chamdothe
6. Kaziputa: Mnyamata wokonda kumuzunza Chamdothe kumasewera 7. Dama: Mmodzi wa achinyamata kumasewero
8. Puna: Mmodzi wa achinyamata kumasewer
9. Anyamata ndi atsikana am’mudzi
2
Malo mwachidule
1) Kubwalo lamasewero m’mudzi
2) Kunyumba kwa Ndatopa
3) Kumunda
4) Ku Mnjiri: Komwe Kaziputa adamukana Puna ngakhale anali bwenzi lake 5) Kunyanja ku Chiromo: Komwe Angozo adasamukira atathawa Ndatopa 6) Kumtsinje