MAWU OFANANA KALEMBEDWE KOMA OSIYANA MATANTHAUZO (Similar but Different Meanings)
-
Definition: Words that are similar but not identical in meaning.
-
Examples:
-
bala – chilonda bereka mwana
-
bango – chipatso cha mtengo wamango
-
zomera za mtundu wa tsekera – zimene zimamera m’mbali mwa mtsinje ndipo amasokera mphasa
-
bawo – bango lolimbitsa m’mbali mwa mphasa
-
mtundu wa masewero – ochita ndi tinthu tobulungira tonga miyala pansi kapena pathabwa
-
buma – gulumwa (mphumphu ya dothi) yambitsa kukhudza maliro
-
cheza – kambirana nkhani ndi munthu
-
lodza kapena chitira – munthu matsenga
-
kuwala kwa dzuwa likamatuluka kapena likamalowa
-
chifungo – batani(butawo) fungo loyipa
-
chigulu – gulu lalikulu
-
chipangizo chosungiramo mchere
-
chikuta
-
chipala
-
fulu galu goba
-
khoma – chiphimba malo onse
-
nyumba yomwe mwabadwira mwana – nsomba yayikulu yopanda mamba phulusa
-
malo osulira zitsulu monga makasu ndi nkhwangwa chichotsa zinthu zapamwamba
-
kanyama kokhala ndi chigoba pamsana – chipanda chachikulu chosungira madzi chiweto chowuwa choteteza pakhomo
-
makwerero am’kati mwa nkhokwe – msampha woluka ndi bango kapena msungwi wambewa nkhwangwa yosemera m’kati mwa thunthu la mtengo monga pokonza bwato.
-
bowola dzenje pa mtengo
-
chipupa
-
lipira msonkho, menya pamutu ndi nkhonya
-
leza – khululuka
-
ng’amba – zinthu monga nsalu kapena pepala mtizigawo Mulungu
-
lumo
-
linga – mpanda wozungulira malo okhalako anthu kuti atetezeke makamaka kwa adani
-
yesa/pima – kukula kapena kulimba kwachinthu khala pa ulendo/pita kwina kwake
-
likhala ngati
-
Makande – nthaka yakuda yomwe imamata (yonyata) nsungwi zong’amba zokonzera nkhokwe
-
Mamba – makwa a nsomba, mtundu wa njoka
-
Menya – senda/chotsa khungu pa thupi lachinthu monga nyama tema mbamu ya nsima
-
Mphonda Tadza Phata – mwana wagalu
-
chipangizo chopalasira bwato
-
chipatso chonga chipanda chomwe amaphika ngati dzungu iwe, tabwera
-
ife tabwera
-
ima motayanitsa miyendo
-
panidwa chifukwa chodzera pampata wochepa lephera kulowa chifukwa chochepa mpata wolowerapo phando lambewu
-
Zinga – zungulira chinthu kapena malo
-
cheka – pakhosi pachinthu monga chiweto
-