MAWU OTSUTSANA MATANTHAUZO (Antonyms)
-
Definition: Words with opposite meanings.
-
Examples:
-
Fulumira – chedwa
-
Khala – imirira
-
Dalitsa – temberera
-
Bunthitsa – nola
-
bambo – mayi
-
banika – puma
-
chepsa – kuza
-
changu – chizere
-
chakuda – choyera
-
iwala – kumbukira
-
buntha – ithwa
-
dzuka – gona
-
perewera – kwanira
-
mphumi – nkhongo/tsoka
-
penya – tsinzina
-
kuka – mphala
-
kwiya – seka
-
masula – manga
-
makono – kale
-
popa – phwetsa
-
tukumuka – fwapa
-
sanjika – sanjula
-
phula – tereka
-
pungula – wonjeza
-
funya – tambasula
-
funyulula – pinda
-
longa – tulutsa/solola
-
lephera – pambana
-
khuthala – pyapyala
-
lemera – pepuka/sauka
-
kana – vomera
-
pusa – chenjera
-