NTCHITO ZA “TI” M’CHIGANIZO
-
Kukhala mgwirizanitsi wamwininkhani
-
Zitsanzo:
-
Ife tinkavuta tili ana. (We struggled when we were kids.)
-
Timakonda kudya. (We love to eat.)
-
-
-
Kukhala mgwirizanitsi wapamtherankhani
-
Zitsanzo:
-
Mayeso atikhaulitsa. (The tests are stressing us.)
-
Yudasi sadatikonde. (Judah does not love us.)
-
-
-
Kusonyeza gulu la dzina (Indicating a name group)
-
Zitsanzo:
-
Kamwana (child)
-
Tiana (they are children)
-
Kahule (female)
-
Timahule (we are females)
-
-
-
Kukhala mphatikiram’mbuyo woloza (Being a prefix for past action)
-
Zitsanzo:
-
Ndikufuna timatemba tija. (I want those children.)
-
Tinyumba tino adatimanga bwino. (Our houses were built well.)
-
-
-
Kuloza (Being a prefix for ongoing action)
-
Zitsanzo:
-
Tiwanati, timatembati, tiaphunzitsiti. (We are children, we learn.)
-
-
-
Kukhala tsinde (Being an indicator)
-
Zitsanzo:
-
Lofunsira:
-
Mudzatola uti patsikulo? (Which one will you take today?)
-
Adakhala pati? (Where are they?)
-
Ubwera liti? (When will you come?)
-
Kodi muli kupita kuti? (Where are you going?)
-
Adzatenga kati? (Will they take which?)
-
Ndikataye muti? (If I lose the tree?)
-
-
-
-
La mneni
-
Zitsanzo:
-
Akuti moni asewere anu. (They say hello to your players.)
-
Nditi mundimasule. (I say you should free me.)
-
-
-
Loloza
-
Zitsanzo:
-
Ndazembetsa timasawu iti. (Which ones did I reserve?)
-
Ndingatole nawo tinkhuni iti? (Which will I take with the branches?)
-
-