MSCE Chichewa Galamala Form 3 and 4

KUSIYANA KWA “LI” NDI “TI”

  1. “li” amasonyeza m’mene chinthu chilili (indicates the state of something) pamene “ti” amasonyeza kuti ntchito ya mneni yemwe watsatana naye ichitika posachedwapa (indicates that the action of the speaker is happening soon).

    • Zitsanzo:

      • Kamkulu ali bwino. (He is in good condition.) – m’mene alili

      • Muchite zomwe nditi ndikutumeni. (Do what I told you to send me.) – ndikutumeni posachedwapa

  2. “ti” amathandiza pofunsa mafunso (indicates the use of questions)

    • Zitsanzo:

      • Mukuloza pati? (Where are you speaking from?)

      • Walakwa ndi uti? (Who did wrong?)

      • Chakusangalatsani ndi chiti? (What makes you happy?)

error: Content is protected !!
Scroll to Top